Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 1:18 - Buku Lopatulika

18 nawauza aphunzitse ana Ayuda nyimbo iyi ya Uta, onani inalembedwa m'buku la Yasara,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 nawauza aphunzitse ana Ayuda nyimbo iyi ya Uta, onani inalembedwa m'buku la Yasara,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Ndipo adalamula kuti mau a madandaulowo aŵaphunzitse kwa anthu a ku Yuda. Mau ake ndi aŵa, monga adalembedwera m'buku la Yasara.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ndipo analamula kuti anthu a ku Yuda aphunzitsidwe nyimbo ya maliroyi imene yalembedwa mʼbuku la Yasari:

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 1:18
4 Mawu Ofanana  

Yuda, abale ako adzakuyamika iwe; dzanja lako lidzakhala pa khosi la adani ako; ana aamuna a atate wako adzakuweramira.


Ulemerero wako, Israele, unaphedwa pa misanje yako. Ha! Adagwa amphamvu!


Tsikuli munaima pamaso pa Yehova Mulungu wanu mu Horebu muja Yehova anati kwa ine, Ndisonkhanitsire anthu, ndidzawamvetsa mau anga, kuti aphunzire kundiopa Ine masiku ao onse akukhala ndi moyo padziko lapansi, ndi kuti aphunzitse ana ao.


Ndipo dzuwa linalinda, ndi mwezi unaima mpaka anthu adabwezera chilango adani ao. Kodi ichi sichilembedwa m'buku la Yasara? Ndipo dzuwa linakhala pakati pa thambo, losafulumira kulowa ngati tsiku lamphumphu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa