Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Mbiri 8:2 - Buku Lopatulika

2 Solomoni anamanga mizinda imene Huramu adampatsa, nakhalitsamo ana a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Solomoni anamanga midzi imene Huramu adampatsa, nakhalitsamo ana a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Pambuyo pake adamanganso kachiŵiri mizinda imene Huramu adampatsa, nakhazikamo Aisraele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Solomoni anamanganso midzi imene anapatsidwa ndi Hiramu, ndipo anakhazikamo Aisraeli.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 8:2
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Rehobowamu anakhala mu Yerusalemu, namanga mizinda yolimbikiramo mu Yuda.


Ndipo kunali, zitatha zaka makumi awiri m'mene Solomoni anamanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba yakeyake,


Ndipo Solomoni anamuka ku Hamatizoba, naugonjetsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa