2 Mbiri 8:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali, zitatha zaka makumi awiri m'mene Solomoni anamanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba yakeyake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali, zitatha zaka makumi awiri m'mene Solomoni anamanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba yakeyake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ntchito yomanga Nyumba ya Chauta ndi nyumba ya mfumu idamtengera Solomoni zaka makumi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Patatha zaka makumi awiri, ndiye nthawi imene Solomoni anamanga Nyumba ya Mulungu ndi nyumba yake yaufumu, Onani mutuwo |