Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Mbiri 2:9 - Buku Lopatulika

9 ndiko kundikonzera mitengo yambirimbiri; pakuti nyumbayi nditi ndiimange idzakhala yaikulu ndi yodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 ndiko kundikonzera mitengo yambirimbiri; pakuti nyumbayi nditi ndiimange idzakhala yaikulu ndi yodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 kuti andidulire mitengo yochuluka, popeza kuti nyumba imene ndimangeyo idzakhala yaikulu ndi yochititsa kaso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 kuti andipatse matabwa ambiri, chifukwa Nyumba imene ndikumanga iyenera kukhala yayikulu ndi yokongola.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 2:9
5 Mawu Ofanana  

Ndipo munthu yense wopitirira pa nyumba yaitali ino adzadabwa nayo, nadzainyoza, nadzati, Yehova watero chifukwa ninji ndi dziko lino ndi nyumba ino?


Ndipo taonani, ndidzawapatsa anyamata anu otema akulikha mitengo miyeso ya tirigu wopuntha zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya barele zikwi makumi awiri, ndi mitsuko yaikulu ya vinyo zikwi makumi awiri, ndi mitsuko yaikulu ya mafuta zikwi makumi awiri.


Ndipo nyumba nditi ndimangeyi ndi yaikulu; pakuti Mulungu wathu ndiye wamkulu woposa milungu yonse.


Munditumizirenso mitengo yamikungudza, ndi yamlombwa, ndi yambawa, ya ku Lebanoni; pakuti ndidziwa kuti anyamata anu adziwa kutema mitengo mu Lebanoni; ndipo taonani, anyamata anga adzakhala ndi anyamata anu,


Ndi munthu yense wakupita pa nyumba iyi yaitali adzadabwa nayo, nadzati, Yehova anatero ndi dziko lino ndi nyumba ino chifukwa ninji?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa