2 Mbiri 2:8 - Buku Lopatulika8 Munditumizirenso mitengo yamikungudza, ndi yamlombwa, ndi yambawa, ya ku Lebanoni; pakuti ndidziwa kuti anyamata anu adziwa kutema mitengo mu Lebanoni; ndipo taonani, anyamata anga adzakhala ndi anyamata anu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Munditumizirenso mitengo yamikungudza, ndi yamlombwa, ndi yambawa, ya ku Lebanoni; pakuti ndidziwa kuti anyamata anu adziwa kutema mitengo m'Lebanoni; ndipo taonani, anyamata anga adzakhala ndi anyamata anu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Munditumizirenso mitengo ya mkungudza, mitengo ya mlombwa ndiponso matabwa ambaŵa a ku Lebanoni, poti ndikudziŵa kuti anyamata anu amadziŵa kudula mitengo ku Lebanoni. Ndipo anyamata anga adzakhala pamodzi ndi anyamata anu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Munditumizirenso mitengo ya mkungudza, payini ndiponso matabwa a mʼbawa wa ku Lebanoni, pakuti ndikudziwa kuti anthu anu ali ndi luso locheka matabwa kumeneko. Antchito anga adzagwira ntchito pamodzi ndi antchito anu Onani mutuwo |