2 Mbiri 2:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo taonani, ndidzawapatsa anyamata anu otema akulikha mitengo miyeso ya tirigu wopuntha zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya barele zikwi makumi awiri, ndi mitsuko yaikulu ya vinyo zikwi makumi awiri, ndi mitsuko yaikulu ya mafuta zikwi makumi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo taonani, ndidzawapatsa anyamata anu otema akulikha mitengo miyeso ya tirigu wopuntha zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya barele zikwi makumi awiri, ndi mitsuko yaikulu ya vinyo zikwi makumi awiri, ndi mitsuko yaikulu ya mafuta zikwi makumi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Anyamata anu odzadula mitengowo ndidzaŵapatsa tirigu wopunthapuntha wokwanira matani 2,000, barele wokwanira matani 2,000, vinyo wa malitara 440,000, ndiponso mafuta a malitara 440,000.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ine ndidzalipira antchito anu amene adzacheke matabwa matani 1,000 a tirigu wopunthapuntha, matani 2,000 a barele, malita 440,000 a vinyo, ndiponso malita 440,000 a mafuta a olivi.” Onani mutuwo |