2 Mbiri 2:2 - Buku Lopatulika2 Nawerenga Solomoni amuna zikwi khumi mphambu makumi asanu ndi limodzi osenza mirimo, ndi amuna zikwi makumi asanu ndi atatu otema mitengo m'mapiri, ndi zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi kuwayang'anira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Nawerenga Solomoni amuna zikwi khumi mphambu makumi asanu ndi limodzi osenza mirimo, ndi amuna zikwi makumi asanu ndi atatu otema mitengo m'mapiri, ndi zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi kuwayang'anira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono adalemba anthu 70,000 osenza katundu, anthu 80,000 okakumba miyala ku dziko lamapiri, ndiponso akapitao 3,600, oyang'anira anthuwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye analemba ntchito anthu 70,000 onyamula katundu ndi anthu 80,000 okumba miyala ku mapiri ndiponso akapitawo 3,600 oyangʼanira anthuwo. Onani mutuwo |