2 Mafumu 9:4 - Buku Lopatulika4 Pamenepo mnyamatayo, ndiye mneneri, anamuka ku Ramoti Giliyadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pamenepo mnyamatayo, ndiye mneneri, anamuka ku Ramoti Giliyadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Motero mneneriyo adapita ku Ramoti-Giliyadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Choncho mneneri wachinyamatayo anapita ku Ramoti Giliyadi. Onani mutuwo |