Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Mafumu 5:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo analowa wina, nauza mbuye wake, kuti, Buthulo lofuma ku dziko la Israele lanena zakutizakuti.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo analowa wina, nauza mbuye wake, kuti, Buthulo lofuma ku dziko la Israele lanena zakutizakuti.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Naamani atamva zimene adaanena mtsikana uja, adapita kwa mfumu nakaiuza kuti, “Mtsikana amene tidakagwira ku Israele uja wanena kuti ati ndipite ku Samariya, kuti mneneri wakumeneko akandichize.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Naamani anapita kwa mbuye wake kukamuwuza zomwe mtsikana wochokera ku Israeli ananena.

Onani mutuwo Koperani




2 Mafumu 5:4
8 Mawu Ofanana  

Nati uyu kwa mbuyake wamkazi, Mbuye wanga akadakhala kwa mneneri ali mu Samariya, akadamchiritsa khate lake.


Pamenepo mfumu ya Aramu inati, Tiye, muka, ndidzatumiza kalata kwa mfumu ya Israele. Pamenepo anachoka, atatenga siliva matalente khumi, ndi golide masekeli zikwi zisanu ndi chimodzi, ndi zovala zakusintha khumi.


Ndipo sanamlole, koma ananena naye, Muka kwanu kwa abale ako, nuwauze zinthu zazikulu anakuchitira Ambuye, ndi kuti anakuchitira chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa