2 Mafumu 4:5 - Buku Lopatulika5 Pamenepo anamchokera, nadzitsekera yekha ndi ana ake aamuna; iwo namtengera zotengerazo, iye namatsanulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamenepo anamchokera, nadzitsekera yekha ndi ana ake amuna; iwo namtengera zotengerazo, iye namatsanulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mai uja adachoka kwa Elisayo, nakadzitsekera ndi ana ake aŵiri aja. Tsono iyeyo ankati akathira mafuta m'mbiya nidzaza, ana ake ankabwera ndi mbiya ina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mayi uja anachoka kwa Elisa nakadzitsekera ndi ana ake. Anthu anabweretsa mitsuko kwa iye ndipo ankathiramo mafuta. Onani mutuwo |