2 Mafumu 3:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Mesa mfumu ya Mowabu anali mwini nkhosa, akapereka kwa mfumu ya Israele ubweya wa anaankhosa zikwi zana limodzi, ndi wa mphongo zikwi zana limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Mesa mfumu ya Mowabu anali mwini nkhosa, akapereka kwa mfumu ya Israele ubweya wa anaankhosa zikwi zana limodzi, ndi wa mphongo zikwi zana limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kale Mesa, mfumu ya Amowabu, ankaŵeta nkhosa. Ndipo chaka ndi chaka ankapereka ngati msonkho kwa mfumu ya Israele anaankhosa okwanira 100,000, ndiponso ubweya wa nkhosa zamphongo 100,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Tsono Mesa, mfumu ya ku Mowabu ankaweta nkhosa, ndipo iye ankayenera kumapereka kwa mfumu ya ku Israeli chaka ndi chaka ana ankhosa onenepa okwanira 100,000 pamodzi ndi ubweya wankhosa 100,000 zazimuna. Onani mutuwo |