2 Mafumu 3:5 - Buku Lopatulika5 Koma kunachitika, atafa Ahabu mfumu ya Mowabu anapandukana ndi mfumu ya Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Koma kunachitika, atafa Ahabu mfumu ya Mowabu anapandukana ndi mfumu ya Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Koma Ahabu atamwalira, mfumu ya Amowabuyo idagalukira mfumu ya ku Israele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Koma atamwalira Ahabu, mfumu ya ku Mowabu inawukira mfumu ya ku Israeli. Onani mutuwo |