2 Mafumu 1:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo mithenga inabwerera kwa iye, nanena nayo, Mwabwerera chifukwa ninji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo mithenga inabwerera kwa iye, nanena nayo, Mwabwerera chifukwa ninji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Amithenga aja adabwerera kwa mfumu. Tsono mfumuyo idaŵafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwabwerera?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Amithenga aja atabwerera kwa mfumu, mfumuyo inawafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwabwerera?” Onani mutuwo |
Ndipo inanena naye, Munthu anakwera kukomana nafe, nati kwa ife, Kabwerereni kwa mfumu imene inakutumani inu, nimunene nayo, Atero Yehova, Kodi ndi popeza palibe Mulungu mwa Israele, kuti ulikutuma kukafunsira kwa Baala-Zebubi mulungu wa ku Ekeroni? Chifukwa chake sudzatsika pakama pamene wakwerapo, koma udzafa ndithu.