2 Akorinto 8:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti monga mwa mphamvu yao, ndichitapo umboni, inde koposa mphamvu yao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti monga mwa mphamvu yao, ndichitapo umboni, inde koposa mphamvu yao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ine ndikuŵachitira umboni kuti adapereka monga adathera, ngakhalenso mopitirira pamenepo poyerekeza ndi chuma chao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Motero ndikuchitira umboni kuti anapereka mmene akanathera, ndipo mwinanso kuposera mmene akathera kupereka. Anapereka mosakakamizidwa, Onani mutuwo |