2 Akorinto 8:4 - Buku Lopatulika4 anachita eni ake, natiumiriza ndi kutidandaulira za chisomocho, ndi za chiyanjano cha utumiki wa kwa oyera mtima; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 anachita eni ake, natiumiriza ndi kutidandaulira za chisomocho, ndi za chiyanjano cha utumiki wa kwa oyera mtima; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Popanda wina aliyense woŵakakamiza adatipempha, natiwumiriza kuti tiŵapatse mwai woti nawonso athandize anthu a Mulungu a ku Yudeya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 ndipo anatipempha motiwumiriza kuti tiwapatse mwayi woti nawonso athandize anthu oyera mtima a ku Yudeya. Onani mutuwo |