2 Akorinto 8:21 - Buku Lopatulika21 pakuti tikonzeratu zinthu zokoma, si pamaso pa Ambuye pokha, komanso pamaso pa anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 pakuti tikonzeratu zinthu zokoma, si pamaso pa Ambuye pokha, komanso pamaso pa anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ifetu tikufuna kuchita zabwino, osati pamaso pa Ambuye pokha, komanso pamaso pa anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pakuti tikuyesetsa kuchita zolondola, osati pamaso pa Ambuye pokha komanso pamaso pa anthu. Onani mutuwo |