2 Akorinto 8:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo tinatumiza mbale wathu awaperekeze iwo, amene tamtsimikizira kawirikawiri ali wakhama m'zinthu zambiri, koma tsopano wa khama loposatu ndi kulimbika kwakukulu kumene ali nako kwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo tinatumiza mbale wathu awaperekeze iwo, amene tamtsimikizira kawirikawiri ali wakhama m'zinthu zambiri, koma tsopano wa khama loposatu ndi kulimbika kwakukulu kumene ali nako kwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Pamodzi ndi iwowo tikutuma mbale wathu wina. Takhala tikumuyesa kaŵirikaŵiri, ndipo tampeza kuti ndi wachangu ndithu pa zinthu zambiri. Tsopano akufunitsitsa koposa kuti athandize, popeza kuti amakukhulupirirani kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Kuwonjezera apo, tikuwatumiza pamodzi ndi mʼbale wathu, amene nthawi zambiri watitsimikizira mʼnjira zosiyanasiyana kuti ndi wachangu ndiponso chifukwa ali ndi chikhulupiriro chachikulu mwa inu. Onani mutuwo |