2 Akorinto 8:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo tatuma pamodzi naye mbaleyo, amene kusimba kwake mu Uthenga Wabwino kuli mu Mipingo yonse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo tatuma pamodzi naye mbaleyo, amene kusimba kwake m'Uthenga Wabwino kuli m'Mipingo yonse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pamodzi ndi iyeyo tikutuma mbale wathu uja, amene mipingo yonse ikumuyamika chifukwa cha ntchito yake yolalika Uthenga Wabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndipo tikumutumiza pamodzi ndi mʼbale amene mipingo yonse yamuyamikira chifukwa cha utumiki wake wa Uthenga Wabwino. Onani mutuwo |