2 Akorinto 8:12 - Buku Lopatulika12 Pakuti ngati chivomerezocho chili pomwepo, munthu alandiridwa monga momwe ali nacho, si monga chimsowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti ngati chivomerezocho chili pomwepo, munthu alandiridwa monga momwe ali nacho, si monga chimsowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Malinga munthu akakhala ndi changu cha kupereka, Mulungu amalandira mokondwa zimene munthuyo ali nazo, ndipo samkakamiza kuti apereke zimene alibe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndipo ngati mtima ofunitsitsa ulipo, mphatsoyo imalandiridwa molingana ndi zimene munthuyo ali nazo, osati zimene alibe. Onani mutuwo |