2 Akorinto 8:11 - Buku Lopatulika11 Koma tsopano tsirizani kuchitaku; kuti monga kunali chivomerezo cha kufunira, koteronso kukhale kutsiriza kwake m'chimene muli nacho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma tsopano tsirizani kuchitaku; kuti monga kunali chivomerezo cha kufunira, koteronso kukhale kutsiriza kwake m'chimene muli nacho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tiyeni tsono muzitsirize. Paja munali ndi changu pofuna kuzichita, muchitenso changu tsopano kuzitsiriza molingana ndi zimene muli nazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsopano tsirizani ntchitoyi, ndipo changu chanu chofunitsitsa kugwira ntchitoyi ndi kuyitsiriza chichitike molingana ndi zimene muli nazo. Onani mutuwo |