2 Akorinto 8:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo m'menemo nditchula choyesa ine; pakuti chimene chipindulira inu, amene munayamba kale chaka chapitachi si kuchita kokha, komanso kufunira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo m'menemo nditchula choyesa ine; pakuti chimene chipindulira inu, amene munayamba kale chaka chapitachi si kuchita kokha, komanso kufunira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pa nkhani imeneyi maganizo anga ndi akuti nkwabwino kuti mutsirize zimene mudayamba kale chaka chathachi, osati kungofuna kuzichita, komanso kuzichita kumene. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo nawa malangizo anga pa zoyenera inu kuchita pa nkhaniyi. Chaka chatha munali oyamba, osati ongofuna kupereka kokha komanso okhala ndi mtima ofuna kupereka. Onani mutuwo |