2 Akorinto 8:13 - Buku Lopatulika13 Pakuti sinditero kuti ena akamasuke, ndi inu musautsidwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pakuti sinditero kuti ena akamasuke, ndi inu musautsidwe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Sindikufuna kunena kuti inuyo muvutike, ena apepukidwe, ai, koma kuti pakhale kulingana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Cholinga chathu sikuti tipeputse ena pamene inuyo mukuvutika, koma kuti pakhale kufanana. Onani mutuwo |