2 Akorinto 8:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo tikudziwitsani, abale, chisomo cha Mulungu chopatsika mwa Mipingo ya ku Masedoniya, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo tikudziwitsani, abale, chisomo cha Mulungu chopatsika mwa Mipingo ya ku Masedoniya, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Abale, tifuna kuti mudziŵe za m'mene Mulungu adadalitsira mipingo ya ku Masedoniya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndipo tsopano, abale, tikufuna kuti mudziwe za chisomo chimene Mulungu wapereka ku mipingo ya ku Makedoniya. Onani mutuwo |