2 Akorinto 7:16 - Buku Lopatulika16 Ndikondwera kuti m'zonse ndilimbika mtima za inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndikondwera kuti m'zonse ndilimbika mtima za inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndikukondwa kuti ndingathe kukukhulupirirani pa zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndine wokondwa kuti ndingathe kukukhulupirirani pa zonse. Onani mutuwo |