2 Akorinto 3:16 - Buku Lopatulika16 Koma pamene akatembenukira kwa Ambuye, chophimbacho chichotsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma pamene akatembenukira kwa Mulungu, chophimbacho chichotsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma munthu akatembenukira kwa Ambuye, chophimbacho chimachotsedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma pamene aliyense atembenukira kwa Ambuye, “chophimbacho chimachotsedwa.” Onani mutuwo |