Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Akorinto 3:15 - Buku Lopatulika

15 Koma kufikira lero, pamene awerengedwa Mose, chophimba chigona pamtima pao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Koma kufikira lero, pamene awerengedwa Mose, chophimba chigona pamtima pao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Ndithu, mpaka lero lino nthaŵi zonse akamaŵerenga Malamulo a Mose, chophimba chija chimaphimbabe mitima yao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Ngakhale lero lomwe lino akuwerenga mabuku a Mose pali chophimbabe mitima yawo.

Onani mutuwo Koperani




2 Akorinto 3:15
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Iye adzaononga m'phiri limeneli chophimba nkhope chovundikira mitundu yonse ya anthu, ndi nsalu yokuta amitundu onse.


koma mitima yao inaumitsidwa; pakuti kufikira lero lomwe lino, pa kuwerenga kwa pangano lakale chophimba chomwechi chikhalabe chosavundukuka, chimene chilikuchotsedwa mwa Khristu.


Koma pamene akatembenukira kwa Ambuye, chophimbacho chichotsedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa