Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Akorinto 2:8 - Buku Lopatulika

8 Chifukwa chake ndikupemphani inu kuti mumtsimikizire ameneyo chikondi chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Chifukwa chake ndikupemphani inu kuti mumtsimikizire ameneyo chikondi chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Nchifukwa chake ndikukupemphani kuti mumtsimikizirenso kuti mumamkonda ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Choncho ndikukupemphani kuti mutsimikizire chikondi chanu pa iye.

Onani mutuwo Koperani




2 Akorinto 2:8
6 Mawu Ofanana  

kotero kwina kuti inu mumkhululukire ndi kumtonthoza, kuti wotereyo akakamizidwe ndi chisoni chochulukacho.


Pakuti chifukwa cha ichi ndalembanso, kuti ndidziwe mayesedwe anu, ngati muli omvera m'zonse.


Pakuti adakuitanani inu, abale, mukhale mfulu; chokhacho musachite nao ufulu wanu chothandizira thupi, komatu mwachikondi chitiranani ukapolo.


Chifukwa chake, monga tili nayo nyengo, tichitire onse chokoma, koma makamaka iwo a pa banja la chikhulupiriro.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa