2 Akorinto 2:7 - Buku Lopatulika7 kotero kwina kuti inu mumkhululukire ndi kumtonthoza, kuti wotereyo akakamizidwe ndi chisoni chochulukacho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 kotero kwina kuti inu mumkhululukire ndi kumtonthoza, kuti wotereyo akakamizidwe ndi chisoni chochulukacho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono makamaka nkwabwino mumkhululukire ndi kumlimbitsa mtima, kuwopa kuti angamve chisoni chachikulu chomtayitsa mtima kotheratu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mʼmalo mwake tsono, muyenera kumukhululukira ndi kumulimbikitsa mtima kuti asamve chisoni choposa muyeso, angataye mtima. Onani mutuwo |