2 Akorinto 2:6 - Buku Lopatulika6 Kwa wotereyo chilango ichi chidachitika ndi ambiri chikwanira; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kwa wotereyo chilango ichi chidachitika ndi ambiri chikwanira; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Munthu woteroyo, pafupi nonse mwamtsutsa, choncho chilangocho nchokwanira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Chilango chimene ambiri a inu mwamupatsa munthu ameneyu nʼchokwanira. Onani mutuwo |
Pakuti, taonani, ichi chomwe, chakuti mudamvetsedwa chisoni cha kwa Mulungu, khama lalikulu lanji chidalichita mwa inu, komanso chodzikonza, komanso mkwiyo, komanso mantha, komanso kukhumbitsa komanso changu, komanso kubwezera chilango! M'zonse munadzitsimikizira nokha kuti muli oyera mtima m'menemo.