2 Akorinto 2:5 - Buku Lopatulika5 Koma ngati wina wachititsa chisoni, sanachititse chisoni ine, koma pena (kuti ndisasenzetse) inu nonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Koma ngati wina wachititsa chisoni, sanachititsa chisoni ine, koma pena (kuti ndisasenzetse) inu nonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ngati wina aliyense adachita kanthu kolasa mtima, si ineyo amene adalasa mtima, koma pang'ono ponse adalasako nonsenu, kunenatu mosakulitsa nkhani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Koma ngati wina wamvetsa chisoni, sanamvetse chisoni ine ndekha, koma koposa mosawonjezera wakhumudwitsa nonsenu, kunenatu mosawonjezera. Onani mutuwo |