2 Akorinto 2:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti ngati ine ndimvetsa inu chisoni, ndaninso amene adzandikondweretsa ine, koma iye amene ndammvetsa chisoni? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti ngati ine ndimvetsa inu chisoni, ndaninso amene adzandikondweretsa ine, koma iye amene ndammvetsa chisoni? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ngati ndine amene ndikukupweteketsani mtima, nanga ineyo adzandisangalatsa ndani, kodi si yemweyo amene ndidampweteketsa mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pakuti ngati ndikumvetsani chisoni, kodi angandisangalatse ndani, kupatula inuyo amene ndakumvetsani chisoni? Onani mutuwo |