Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Akorinto 2:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Pakuti ngati ndikumvetsani chisoni, kodi angandisangalatse ndani, kupatula inuyo amene ndakumvetsani chisoni?

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Pakuti ngati ine ndimvetsa inu chisoni, ndaninso amene adzandikondweretsa ine, koma iye amene ndammvetsa chisoni?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Pakuti ngati ine ndimvetsa inu chisoni, ndaninso amene adzandikondweretsa ine, koma iye amene ndammvetsa chisoni?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Ngati ndine amene ndikukupweteketsani mtima, nanga ineyo adzandisangalatsa ndani, kodi si yemweyo amene ndidampweteketsa mtima.

Onani mutuwo Koperani




2 Akorinto 2:2
6 Mawu Ofanana  

Mnyamatayo atamva zimenezi, anachoka mokhumudwa, chifukwa anali ndi chuma chambiri.


Kondwani pamodzi ndi amene akukondwa ndipo lirani ndi amene akulira.


Ngati chiwalo chimodzi chikumva kuwawa, ziwalo zonse zimamvanso kuwawa. Ngati chiwalo chimodzi chilandira ulemu, ziwalo zonse zimakondwera nawo.


Monga mwamva pangʼono chabe, ndikuyembekeza kuti mudzamvetsa kwenikweni, kuti mutha kutinyadira monga ife tidzakunyadirani, pa tsiku la Ambuye Yesu.


Ndani ali wofowoka, ine wosakhala naye mʼkufowoka kwakeko? Ndani amene mnzake amuchimwitsa, ine wosavutika mu mtima?


Ngakhale kalata yanga ija inakupwetekani mtima, sindikudandaula kuti ndinalemberanji. Ngakhale zinandikhudza, ndikudziwa kuti kalata yanga inakupwetekani, koma kwa kanthawi kochepa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa