2 Akorinto 11:9 - Buku Lopatulika9 ndipo pakukhala nanu, ndi kusowa, sindinasaukitse munthu aliyense; pakuti abale akuchokera ku Masedoniya, anakwaniritsa kusowa kwanga; ndipo m'zonse ndinachenjera ndekha, ndisalemetse inu, ndipo ndidzachenjerapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndipo pakukhala nanu, ndi kusowa, sindinasaukitsa munthu aliyense; pakuti abale akuchokera ku Masedoniya, anakwaniritsa kusowa kwanga; ndipo m'zonse ndinachenjera ndekha, ndisalemetse inu, ndipo ndidzachenjerapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndipo pamene ndinali kwanuko, nditasoŵa kanthu, sindidavute aliyense, pakuti abale ena ochokera ku Masedoniya adaandipatsa zonse zimene ndinkasoŵa. Pa zonse ndinkasamala kwambiri kuti ndisakhale ngati katundu wokulemerani, ndipo ndidzapitirirabe kutero. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo pamene ndinali pakati panu, nditasowa kanthu, sindinalemetse munthu aliyense, pakuti abale ena amene anachokera ku Makedoniya anandipatsa zonse zimene ndinkazisowa. Ndayesetsa kuti ndisakhale cholemetsa kwa inu mʼnjira ina iliyonse, ndipo ndidzapitiriza kutero. Onani mutuwo |