2 Akorinto 11:8 - Buku Lopatulika8 Ndinalanda za Mipingo ina, ndi kulandira kwa iwo kulipira kuti ndikatumikire inu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndinalanda za Mipingo ina, ndi kulandira kwa iwo kulipira kuti ndikatumikire inu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pakulandira zondithandiza kuchokera ku mipingo ina, ndidachita ngati kuŵalanda zao kuti ndikutumikireni inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndinkalanda mipingo ina pomalandira thandizo kwa iwo kuti ndikutumikireni. Onani mutuwo |