2 Akorinto 11:7 - Buku Lopatulika7 Kodi ndachimwa podzichepetsa ndekha, kuti inu mukakwezedwe, popeza ndinalalikira kwa inu Uthenga Wabwino wa Mulungu mwaufulu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Kodi ndachimwa podzichepetsa ndekha, kuti inu mukakwezedwe, popeza ndinalalikira kwa inu Uthenga Wabwino wa Mulungu mwaufulu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ndidadzitsitsa ndekha ineyo, kuti inu mukule. Ndidakulalikirani mwaulere Uthenga Wabwino wa Mulungu. Kodi ndiye kuti pakutero ndidalakwa? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kodi linali tchimo kwa ine kudzichepetsa nʼcholinga chakuti ndikukwezeni pamene ndinkalalikira Uthenga Wabwino wa Mulungu kwa inu mwaulere? Onani mutuwo |