2 Akorinto 11:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo ndingakhale ndili wosaphunzira m'manenedwe, koma sinditero m'chidziwitso, koma m'zonse tachionetsa kwa inu mwa anthu onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo ndingakhale ndili wosaphunzira m'manenedwe, koma sinditero m'chidziwitso, koma m'zonse tachionetsa kwa inu mwa anthu onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ngakhale ndine mbuli pa luso lolankhula, koma pa nzeru ndiye ai. Zimenezi ndidakuwonetsani kaŵirikaŵiri pa zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Mwina ndikhoza kukhala wosaphunzitsidwa kayankhulidwe, koma ndili ndi chidziwitso. Izi tinakufotokozerani momveka bwinobwino. Onani mutuwo |