2 Akorinto 11:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti ndiyesa kuti sindinaperewere konse ndi atumwi oposatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti ndiyesa kuti sindinaperewera konse ndi atumwi oposatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ndikuganiza kuti atumwi anu apamwambawo sandiposa ine pa kanthu kalikonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Komatu sindikuganiza kuti ndine wotsika kwambiri kwa “atumwi apamwamba.” Onani mutuwo |