2 Akorinto 10:11 - Buku Lopatulika11 Woteroyo ayese ichi kuti monga tili ife ndi mau mwa makalata, pokhala palibe ife, tili oterenso m'machitidwe pokhala tili pomwepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Woteroyo ayese ichi kuti monga tili ife ndi mau mwa akalata, pokhala palibe ife, tili oterenso m'machitidwe pokhala tili pomwepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Anthu oganiza zotere, adziŵe kuti palibe kusiyana pakati pa zimene timanena m'makalata pamene tili nanu kutali ndi zimene timachita tikakhala nanu pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Anthu oterewa ayenera kuzindikira kuti zomwe timalemba mʼmakalata tili kutali ndi zomwe tidzakhale tili komweko. Onani mutuwo |