2 Akorinto 1:14 - Buku Lopatulika14 monganso munativomerezera ife pena, kuti ife ndife kudzitamandira kwanu, monga momwe inunso muli kudzitamandira kwathu m'tsiku la Ambuye wathu Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 monganso munativomerezera ife pena, kuti ife ndife kudzitamandira kwanu, monga momwe inunso muli kudzitamandira kwathu m'tsiku la Ambuye wathu Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 monga mwayamba kale kutidziŵa pang'ono, mudzatidziŵa kwenikweni, ndiye kuti pa tsiku la Ambuye Yesu mudzatha kutinyadira ife, monga momwe ifenso tidzakunyadirani inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Monga mwamva pangʼono chabe, ndikuyembekeza kuti mudzamvetsa kwenikweni, kuti mutha kutinyadira monga ife tidzakunyadirani, pa tsiku la Ambuye Yesu. Onani mutuwo |