2 Akorinto 1:13 - Buku Lopatulika13 Pakuti sitilemba kwa inu zina, koma zimene muwerenga, kapenanso muvomereza; ndipo ndiyembekeza kuti mudzavomereza kufikira chimaliziro; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pakuti sitilemba kwa inu zina, koma zimene muwerenga, kapenanso muvomereza; ndipo ndiyembekeza kuti mudzavomereza kufikira chimaliziro; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Timakulemberani zokhazokha zimene mungathe kuziŵerenga ndi kuzimvetsa bwino. Ndikhulupirira kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pakuti sitikukulemberani zoti simungawerenge kapena kumvetsetsa. Onani mutuwo |