2 Akorinto 1:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo m'kulimbika kumene ndinafuna kudza kwa inu kale, kuti mukakhale nacho chisomo chachiwiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo m'kulimbika kumene ndinafuna kudza kwa inu kale, kuti mukakhale nacho chisomo chachiwiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Popeza kuti pa zimenezi ndinali wotsimikiza ndithu, ndidaaganiza zoti ndiyambe ndafika kwanuko. Ndidaafuna kuti mulandire madalitso paŵiri: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Popeza ndinatsimikiza mtima za ichi, nʼchifukwa chake ndinafuna kuti poyamba, ndidzakuchezereni kuti mupindule pawiri. Onani mutuwo |