1 Timoteyo 3:4 - Buku Lopatulika4 woweruza bwino nyumba yake ya iye yekha, wakukhala nao ana ake omvera iye ndi kulemekezeka konse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 woweruza bwino nyumba yake ya iye yekha, wakukhala nao ana ake omvera iye ndi kulemekezeka konse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Akhale wodziŵa kuyendetsa bwino banja lake, ndi kulera bwino ana ake, kuti akhale omvera ndi aulemu kwenikweni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Akhale wodziwa kusamala bwino banja lake ndi kulera ana ake bwino, kuti akhale omvera ndi aulemu weniweni. Onani mutuwo |