1 Timoteyo 2:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti ichi nchokoma ndi cholandirika pamaso pa Mulungu Mpulumutsi wathu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti ichi nchokoma ndi cholandirika pamaso pa Mulungu Mpulumutsi wathu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Zimenezi nzabwino ndi zokondweretsa pamaso pa Mulungu, Mpulumutsi wathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Izi ndi zabwino ndipo zimakondweretsa Mulungu Mpulumutsi wathu, Onani mutuwo |