1 Samueli 9:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo pamene anatsika kumsanje kulowanso kumzinda, iye anakamba ndi Saulo pamwamba pa nyumba yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo pamene anatsika kumsanje kulowanso kumudzi, iye anakamba ndi Saulo pamwamba pa nyumba yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ndipo pamene adatsika kuchokera kukachisi kuja kukaloŵa mu mzinda, adamukonzera Saulo pogona pamwamba pa denga, ndipo iye adagona pamenepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Atatsika kuchoka ku phiri kuja, Samueli anamukonzera Sauli malo ogona pa denga la nyumba yake, ndipo Sauli anagona pamenepo. Onani mutuwo |