1 Samueli 9:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo Samuele ananena ndi wophika, Tenga nyama ndinakupatsa, ndi kuti, Ibakhala ndi iwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo Samuele ananena ndi wophika, Tenga nyama ndinakupatsa, ndi kuti, Ibakhala ndi iwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Adauza wophika kuti, “Bwera nayo nthuli yanyama ija ndidaakupatsayi. Paja ndidaakuuza kuti uiike pambali.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Tsono Samueli anati kwa wophika, “Bwera nayo nyama imene ndinakupatsa, imene ndinakuwuza kuti uyisunge pambali.” Onani mutuwo |