1 Samueli 9:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Samuele anatenga Saulo ndi mnyamata wake, napita nao ku chipinda cha alendo, nawakhalitsa pamalo a ulemu pakati pa oitanidwa onse; ndiwo anthu monga makumi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Samuele anatenga Saulo ndi mnyamata wake, napita nao ku chipinda cha alendo, nawakhalitsa pa malo a ulemu pakati pa oitanidwa onse; ndiwo anthu monga makumi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Tsono Samuele adatenga Saulo ndi mnyamata wake uja, ndipo adaloŵa nawo m'chipinda chachikulu, naŵapatsa malo kutsogolo kwa anthu oitanidwa, amene onse pamodzi anali ngati anthu makumi atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ndipo Samueli anatenga Sauli ndi mnyamata wake uja ndi kulowa nawo mʼchipinda chachikulu ndipo anawakhazika kutsogolo kwa anthu oyitanidwa. Onse pamodzi analipo anthu makumi atatu. Onani mutuwo |