Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 9:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo Yehova anaululiratu m'khutu la Samuele dzulo lake la tsiku limene Saulo anabwera, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo Yehova anaululiratu m'khutu la Samuele dzulo lake la tsiku limene Saulo anabwera, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Koma chadzulo, Saulo asanabwere, nkuti Chauta atamdziŵitsiratu Samuele kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Koma chadzulo lake Sauli asanafike, Yehova anali atamuwuza kale Samueli za zimenezi kuti,

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 9:15
13 Mawu Ofanana  

Pakuti inu, Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele, munawulula kwa mnyamata wanu kuti, Ndidzakumangira iwe nyumba; chifukwa chake mnyamata wanu analimbika mtima kupemphera pemphero ili kwa Inu.


pamenepo atsegula makutu a anthu, nakomera chizindikiro chilangizo chao;


Chinsinsi cha Yehova chili kwa iwo akumuopa Iye; ndipo adzawadziwitsa pangano lake.


Pakuti Ambuye Yehova sadzachita kanthu osawulula chinsinsi chake kwa atumiki ake aneneri.


Ndipo kuyambira pamenepo anapempha mfumu; ndipo Mulungu anawapatsa Saulo mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini, zaka makumi anai.


Pakuti anaimirira kwa ine usiku walero mngelo wa Mulungu amene ndili wake, amenenso ndimtumikira,


Ndipo Samuele ananena ndi Saulo, Yehova ananditumiza ine kukudzozani mukhale mfumu ya anthu ake Aisraele; chifukwa chake tsono mumvere kunena kwa mau a Yehova.


Namyankha, Usatero iai, sudzafa; ona, atate wanga sachita kanthu kakakulu kapena kakang'ono wosandidziwitsa ine; atate wanga adzandibisiranji chinthu chimenechi? Si kutero ai.


Ndipo Yehova anaonekanso mu Silo, pakuti Yehova anadziwulula kwa Samuele ku Silo, mwa mau a Yehova.


Ndipo iwowa anakwera kumzinda; ndipo m'mene analowa m'mzindamo, onani, Samuele anatulukira pali iwo, kuti akakwere kumsanje.


Ndipo pamene Samuele anaona Saulo, Yehova anati kwa iye, Ona munthu amene ndinakuuza za iye! Ameneyu adzaweruza anthu anga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa