1 Samueli 9:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo iwowa anakwera kumzinda; ndipo m'mene analowa m'mzindamo, onani, Samuele anatulukira pali iwo, kuti akakwere kumsanje. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo iwowa anakwera kumudzi; ndipo m'mene analowa m'mudzimo, onani, Samuele anatulukira pali iwo, kuti akakwere kumsanje. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Choncho adapita kumzindako. Poloŵa mumzindamo, adaona Samuele akutuluka kumene, alikudza kwa iwo pa njira yopita kukachisi kuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Choncho anapita ku mzinda kuja. Akulowa mu mzindamo, anaona Samueli akutuluka mu mzindamo akubwera kumene kunali iwo, koma amapita ku phiri, ku malo wopatulika. Onani mutuwo |