1 Samueli 9:11 - Buku Lopatulika11 Pakukwera kumzindako anapeza anthu aakazi alikutuluka kuti akatunge madzi, nanena nao, Mlauliyo alipo kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pakukwera kumudziko anapeza anthu akazi alikutuluka kuti akatunge madzi, nanena nao, Mlauliyo alipo kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pamene ankakwera phiri kupita kumzindako, adakumana ndi atsikana akutuluka mumzindamo kukatunga madzi, ndipo adaŵafunsa kuti, “Kodi mlosi uja alipo?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Akukwera phiri kupita ku mzindawo anakumana ndi atsikana akutuluka mu mzindamo kukatunga madzi, ndipo anawafunsa kuti, “Kodi mlosi uja alipo?” Onani mutuwo |