1 Samueli 9:10 - Buku Lopatulika10 Pamenepo Saulo anati kwa mnyamata wake, Wanena bwino; tiye tipite. Chomwecho iwowa anapita kumzinda kumene kunali munthu wa Mulunguyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pamenepo Saulo anati kwa mnyamata wake, Wanena bwino; tiye tipite. Chomwecho iwowa anapita kumudzi kumene kunali munthu wa Mulunguyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono Saulo adauza mnyamata wakeyo kuti, “Chabwino. Tiye tizipita.” Choncho adapita kumzinda kumene kunali munthu wa Mulunguko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Tsono Sauli anawuza mnyamata wake kuti, “Chabwino, tiye tipite.” Ndipo ananyamuka kupita ku mzinda umene kunali munthu wa Mulunguyo. Onani mutuwo |